Ezekieli 20:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana+ ku mbali ya kum’mwera ndipo ulankhule+ mawu onena za kumeneko. Ulosere kunkhalango ya dziko la kum’mwera.
46 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana+ ku mbali ya kum’mwera ndipo ulankhule+ mawu onena za kumeneko. Ulosere kunkhalango ya dziko la kum’mwera.