Amosi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzatumiza moto ku Mowabu, ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Kerioti.+ Mowabu adzafa pakati pa phokoso la asilikali, kulira kwa chizindikiro chochenjeza ndiponso lipenga la nyanga ya nkhosa.+
2 Ndidzatumiza moto ku Mowabu, ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za Kerioti.+ Mowabu adzafa pakati pa phokoso la asilikali, kulira kwa chizindikiro chochenjeza ndiponso lipenga la nyanga ya nkhosa.+