Amosi 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho ndidzatumiza moto ku Mowabu,Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za Kerioti.+Mowabu adzafa pakati pa phokoso,Pakati pa mfuu yankhondo ndiponso kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa.+
2 Choncho ndidzatumiza moto ku Mowabu,Ndipo udzawotcheratu nsanja zolimba za Kerioti.+Mowabu adzafa pakati pa phokoso,Pakati pa mfuu yankhondo ndiponso kulira kwa lipenga la nyanga ya nkhosa.+