Yesaya 59:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe amene akufuula mwachilungamo,+ ndipo palibe amene amalankhula mokhulupirika akapita kukhoti. Anthu inu mukukhulupirira zinthu zachabechabe+ ndipo mukulankhula zopanda pake.+ Mwatenga pakati pa mavuto ndipo mwabereka zopweteka.+
4 Palibe amene akufuula mwachilungamo,+ ndipo palibe amene amalankhula mokhulupirika akapita kukhoti. Anthu inu mukukhulupirira zinthu zachabechabe+ ndipo mukulankhula zopanda pake.+ Mwatenga pakati pa mavuto ndipo mwabereka zopweteka.+