Salimo 62:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+ Yesaya 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero Woyera wa Isiraeli wanena kuti: “Anthu inu mwakana mawu anga+ n’kumadalira kuba mwachinyengo. Mukudalira zinthu zachinyengo ndipo mukukhulupirira zinthu zimenezo.+
10 Musadalire chizolowezi chobera ena mwachinyengo,+Ndipo musakhale wachabechabe chifukwa chochita uchifwamba.+Ngati chuma chanu chachuluka, mtima wanu wonse usakhale pachumacho.+
12 Chotero Woyera wa Isiraeli wanena kuti: “Anthu inu mwakana mawu anga+ n’kumadalira kuba mwachinyengo. Mukudalira zinthu zachinyengo ndipo mukukhulupirira zinthu zimenezo.+