2 Mbiri 28:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pa nthawi imene Mfumu Ahazi inali kusautsidwa, inawonjezera kuchita zosakhulupirika kwa Yehova.+