Salimo 52:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+ Miyambo 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+
7 Munthu wamphamvu wotere sadalira Mulungu monga malo ake achitetezo,+Koma amadalira kuchuluka kwa chuma chake,+Ndipo chitetezo chake amachipeza m’mavuto amene iyeyo amawachititsa.+
3 Kupusa kwa munthu wochokera kufumbi n’kumene kumapotoza njira yake,+ choncho mtima wake umakwiyira Yehova.+