1 Samueli 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Samueli anauza Sauli kuti: “Wachita chinthu chopusa.+ Sunatsatire lamulo+ limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanatsatira lamulo limeneli, Yehova akanalimbitsa ufumu wako pa Isiraeli mpaka kalekale. 1 Mafumu 20:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+ Miyambo 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye adzafa chifukwa chosamvera malangizo,+ ndiponso chifukwa chakuti amasocheretsedwa ndi zopusa zake zochuluka.+ Machitidwe 13:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ayuda ataona khamu la anthulo, anachita nsanje+ ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo anali kulankhula.+
13 Pamenepo Samueli anauza Sauli kuti: “Wachita chinthu chopusa.+ Sunatsatire lamulo+ limene Yehova Mulungu wako anakupatsa.+ Ukanatsatira lamulo limeneli, Yehova akanalimbitsa ufumu wako pa Isiraeli mpaka kalekale.
42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+
23 Iye adzafa chifukwa chosamvera malangizo,+ ndiponso chifukwa chakuti amasocheretsedwa ndi zopusa zake zochuluka.+
45 Ayuda ataona khamu la anthulo, anachita nsanje+ ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo anali kulankhula.+