Yesaya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’tsiku limene Yehova adzakupatseni mpumulo ku ululu wanu, ku nsautso yanu ndi ku ukapolo wowawa umene inu munalimo,+
3 M’tsiku limene Yehova adzakupatseni mpumulo ku ululu wanu, ku nsautso yanu ndi ku ukapolo wowawa umene inu munalimo,+