Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pofika mwezi wa 7,+ ana a Isiraeli anali akukhala m’mizinda yawo. Ndiyeno anthuwo anayamba kusonkhana ku Yerusalemu+ monga munthu mmodzi.+

  • Ezara 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano kwa nthawi yochepa, Yehova Mulungu wathu watikomera mtima+ mwa kutisiyira anthu opulumuka,+ ndiponso mwa kutipatsa malo otetezeka* m’malo ake oyera kuti maso athu awale,+ inu Mulungu wathu, ndi kutitsitsimutsa pang’ono mu ukapolo wathu.+

  • Yesaya 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 M’tsiku limenelo+ ndithu udzanena kuti: “Ndikukuthokozani inu Yehova pakuti ngakhale munandikwiyira, mkwiyo wanu unabwerera pang’onopang’ono+ ndipo munanditonthoza.+

  • Yesaya 32:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Anthu anga adzakhala pamalo amtendere ndi pamalo otetezeka. Adzakhala m’malo abata ndiponso aphee!+

  • Yeremiya 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Koma iwe Yakobo mtumiki wanga usachite mantha, iwe Isiraeli usagwidwe ndi mantha,”+ watero Yehova. “Pakuti ine ndikukupulumutsa kuchokera kutali ndipo ndikupulumutsanso ana ako kuchokera kudziko limene anatengedwa kukakhala akapolo.+ Yakobo adzabwerera ndipo adzakhala mosatekeseka komanso mopanda zosokoneza. Sipadzakhala womuopsa.”+

  • Ezekieli 28:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Nyumba ya Isiraeli sidzalasidwanso ndi cholasa chopweteka+ kapena minga zaululu zochokera kwa onse owazungulira, amene akuwatonza, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena