Yesaya 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Aliyense amene adzapezedwe adzabooledwa ndipo aliyense amene adzagwidwe limodzi ndi anthu ena onse pa nthawiyo, adzaphedwa ndi lupanga.+ Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa,+
15 Aliyense amene adzapezedwe adzabooledwa ndipo aliyense amene adzagwidwe limodzi ndi anthu ena onse pa nthawiyo, adzaphedwa ndi lupanga.+