2 Mafumu 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.
14 Akasidiwo anatenganso ndowa, mafosholo, zozimitsira nyale, makapu, ndi ziwiya zonse+ zamkuwa zimene ansembe anali kugwiritsira ntchito potumikira.