1 Mafumu 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako anapanga mabeseni 10+ amkuwa. Beseni lililonse linali lokwana mitsuko* 40, ndipo linali mikono inayi kukula kwake. Pachotengera chilichonse mwa zotengera 10 zija panali beseni limodzi.
38 Kenako anapanga mabeseni 10+ amkuwa. Beseni lililonse linali lokwana mitsuko* 40, ndipo linali mikono inayi kukula kwake. Pachotengera chilichonse mwa zotengera 10 zija panali beseni limodzi.