Yeremiya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa makamu wanena kuti: “Mosalephera adani adzakunkha otsalira a Isiraeli ngati mmene amakunkhira mphesa.+ Kweza dzanja lako ngati munthu amene akuthyola mphesa panthambi za mtengo wa mpesa.”
9 Yehova wa makamu wanena kuti: “Mosalephera adani adzakunkha otsalira a Isiraeli ngati mmene amakunkhira mphesa.+ Kweza dzanja lako ngati munthu amene akuthyola mphesa panthambi za mtengo wa mpesa.”