Nehemiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malikiya mwana wamwamuna wa Rekabu, kalonga wa chigawo cha Beti-hakeremu,+ anakonza Chipata cha Milu ya Phulusa. Iye anachimanga ndi kuika zitseko zake, akapichi ake ndi mipiringidzo yake.
14 Malikiya mwana wamwamuna wa Rekabu, kalonga wa chigawo cha Beti-hakeremu,+ anakonza Chipata cha Milu ya Phulusa. Iye anachimanga ndi kuika zitseko zake, akapichi ake ndi mipiringidzo yake.