Miyambo 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chotero adzadya zipatso za njira yawo,+ ndipo adzakhuta malangizo awo.+ Yesaya 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+
7 Mapazi awo amangothamangira kukachita zoipa,+ ndipo amafulumira kuti akakhetse magazi osalakwa.+ Maganizo awo ndi opweteka anzawo.+ M’misewu mwawo amangokhalira kusakazana ndi kuwonongana.+