Yesaya 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Taona! Onse okupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akukangana nawe sadzakhalanso ngati kanthu ndipo adzatha.+ Zekariya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+
11 “Taona! Onse okupsera mtima adzachita manyazi ndipo adzanyozeka.+ Anthu amene akukangana nawe sadzakhalanso ngati kanthu ndipo adzatha.+
15 Ndakwiyira kwambiri anthu a mitundu ina amene akukhala mwabata.+ Ndawakwiyira chifukwa chakuti ine ndinangokwiyira anthu anga pang’ono pokha,+ koma anthu amenewa anakulitsa tsoka la anthu angawo.”’+