Yesaya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+ Yeremiya 23:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+ “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova.
3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+
12 “Choncho, njira zawo zidzawakhalira ngati malo oterera+ amdima ndipo adzawakankhira m’njirazo moti adzagwa.”+ “Pakuti ndidzawagwetsera tsoka, tsiku la chilango chawo lidzafika,”+ watero Yehova.