Yesaya 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kubangula kwawo kuli ngati kwa mkango ndipo amabangula ngati mikango yamphamvu.+ Iwo adzabangula n’kugwira nyama. Adzainyamula bwinobwino ndipo sipadzakhala woipulumutsa.+
29 Kubangula kwawo kuli ngati kwa mkango ndipo amabangula ngati mikango yamphamvu.+ Iwo adzabangula n’kugwira nyama. Adzainyamula bwinobwino ndipo sipadzakhala woipulumutsa.+