Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+ Yesaya 42:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma anthu amenewa agwidwa ndipo atengedwa.+ Onsewa anagwera m’maenje ndipo akhala akubisidwa m’ndende.+ Atengedwa popanda wowalanditsa.+ Agwidwa popanda wonena kuti: “Bwererani nawo!”
22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+
22 Koma anthu amenewa agwidwa ndipo atengedwa.+ Onsewa anagwera m’maenje ndipo akhala akubisidwa m’ndende.+ Atengedwa popanda wowalanditsa.+ Agwidwa popanda wonena kuti: “Bwererani nawo!”