Miyambo 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ngakhale utasinja chitsiru mumtondo ndi musi limodzi ndi mbewu, uchitsiru wake sungachichokere.+ Mateyu 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiponso ndikukuuzani kuti, N’chapafupi kuti ngamila ilowe padiso la singano kusiyana n’kuti munthu wolemera alowe mu ufumu wa Mulungu.”+
24 Ndiponso ndikukuuzani kuti, N’chapafupi kuti ngamila ilowe padiso la singano kusiyana n’kuti munthu wolemera alowe mu ufumu wa Mulungu.”+