2 Mbiri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yogometsa,+ pakuti Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.+ Yesaya 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+
5 Nyumba imene ndikumangayi idzakhala yogometsa,+ pakuti Mulungu wathu ndi wamkulu kuposa milungu ina yonse.+
6 M’chaka chimene Mfumu Uziya inamwalira,+ ine ndinaona Yehova+ atakhala pampando wachifumu+ wolemekezeka umene unali pamalo okwezeka, ndipo zovala zake zinadzaza m’kachisi.+