Rute 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma iye powayankha anali kunena kuti: “Musanditchulenso kuti Naomi,* muzinditchula kuti Mara,* chifukwa Wamphamvuyonse+ wachititsa moyo wanga kukhala wowawa kwambiri.+ Yobu 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Sadzalola kuti ndipumeko mpweya wabwino,+Chifukwa akungondikhuthulira zinthu zowawa.
20 Koma iye powayankha anali kunena kuti: “Musanditchulenso kuti Naomi,* muzinditchula kuti Mara,* chifukwa Wamphamvuyonse+ wachititsa moyo wanga kukhala wowawa kwambiri.+