Deuteronomo 28:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+ Miyambo 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kapolo akamalamulira monga mfumu,+ munthu wopusa akakhuta,+ Yesaya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzaika anyamata kuti akhale akalonga awo ndipo anthu ankhanza adzawalamulira.+
43 Mlendo wokhala pakati panu adzapitirizabe kutukuka kukuposani, koma inuyo mudzapitirizabe kutsika pansi.+