Ezekieli 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nena mwambi wokhudza nyumba yopanduka.+ Unene kuti:“‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ika pamoto mphika wakukamwa kwakukulu ndipo uthiremo madzi.+
3 Nena mwambi wokhudza nyumba yopanduka.+ Unene kuti:“‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Ika pamoto mphika wakukamwa kwakukulu ndipo uthiremo madzi.+