Zekariya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Popeza kuti ine ndikawaitana sanali kundimvera,+ iwonso akandiitana sindinali kuwamvera,’+ watero Yehova wa makamu.
13 “‘Popeza kuti ine ndikawaitana sanali kundimvera,+ iwonso akandiitana sindinali kuwamvera,’+ watero Yehova wa makamu.