Zekariya 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Ine ndikawaitana sankandimvera,+ choncho iwonso akandiitana sindinkawamvera,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
13 “‘Ine ndikawaitana sankandimvera,+ choncho iwonso akandiitana sindinkawamvera,’+ watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.