Yesaya 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+ Maliro 3:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Mwadzitchinga ndi mtambo kuti pemphero lathu lisafike kwa inu.+
15 Ndipo mukatambasula manja anu,Ndimakubisirani maso anga.+ Ngakhale mupereke mapemphero ambiri,+Ine sindimvetsera.+Manja anu adzaza magazi.+