Yeremiya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+ Ezekieli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ineyo ndidzachitapo kanthu mwaukali.+ Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Iwo adzandiitana mofuula, koma ine sindidzamva.”+
5 Ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima, ndiponso ndili ndi ukali waukulu.+
18 Choncho ineyo ndidzachitapo kanthu mwaukali.+ Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Iwo adzandiitana mofuula, koma ine sindidzamva.”+