-
Ezekieli 12:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Anthu a m’dzikoli uwauze kuti, ‘Izi n’zimene Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kwa anthu okhala mu Yerusalemu, okhala m’dziko la Isiraeli:+ “Adzadya chakudya ndi nkhawa ndipo adzamwa madzi ndi mantha, pakuti dzikolo lidzakhala bwinja.+ Zinthu zonse za mmenemo zidzachotsedwa chifukwa cha zinthu zachiwawa zimene anthu onse okhala mmenemo akuchita.+
-