Ezekieli 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+ Ezekieli 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga.+ Ndidzasolola lupanga langa m’chimake+ ndi kupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.+
2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+
3 Uuze dziko la Isiraeli kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Ine ndidzakulanga.+ Ndidzasolola lupanga langa m’chimake+ ndi kupha anthu ako olungama ndiponso anthu ako oipa.+