Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja. Ezekieli 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “‘Kapena nditati ndibweretse lupanga m’dzikolo,+ n’kunena kuti: “M’dzikolo mudutse lupanga,” ine n’kuphamo anthu ndi ziweto,+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukupitikitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja,+ ndipo mizinda yanu idzawonongedwa ndi kukhala mabwinja.
17 “‘Kapena nditati ndibweretse lupanga m’dzikolo,+ n’kunena kuti: “M’dzikolo mudutse lupanga,” ine n’kuphamo anthu ndi ziweto,+