Yeremiya 25:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo akamwe ndi kudzandira uku ndi uku ndipo akakhale ngati anthu amisala chifukwa cha lupanga limene ndikuwatumizira pakati pawo.”+
16 Iwo akamwe ndi kudzandira uku ndi uku ndipo akakhale ngati anthu amisala chifukwa cha lupanga limene ndikuwatumizira pakati pawo.”+