Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 51:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Babulo wakhala kapu yagolide m’dzanja la Yehova+ ndipo waledzeretsa dziko lonse lapansi.+ Mitundu ya anthu yaledzera ndi vinyo wake.+ N’chifukwa chake mitundu ya anthu ikuchita zinthu zamisala.+

  • Maliro 4:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kondwa ndipo usangalale,+ iwe mwana wamkazi wa Edomu,+ amene ukukhala m’dziko la Uzi.+

      Iwenso kapuyo ikupeza.+ Udzaledzera ndipo anthu adzakuona uli maliseche.+

  • Ezekieli 23:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Iwe udzamwa ndi kugugudiza za m’kapuyo,+ ndipo udzatafuna zidutswa za kapuyo ndi kukhadzula mabere ako.+ “Ine ndanena,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’

  • Nahumu 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Chotero iwenso udzaledzera,+ ndipo udzabisala.+ Iwenso udzafunafuna malo okhala ndi mpanda wolimba kwambiri kuti utetezeke kwa mdani.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena