Yoswa 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mafumu asanu aja anathawa+ n’kukabisala kuphanga la ku Makeda.+ 1 Samueli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.
6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.