Deuteronomo 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+ 1 Samueli 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero, onse awiri anadzionetsera kumudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo Afilisitiwo anayamba kunena kuti: “Taonani Aheberi akutuluka m’maenje amene anabisala.”+
3 kuti, ‘Mverani Aisiraeli inu. Lero mukuyandikira adani anu kuti mumenyane nawo. Mitima yanu isachite mantha.+ Musaope ndipo musathawe mwamantha kapena kunjenjemera chifukwa cha iwo,+
11 Atatero, onse awiri anadzionetsera kumudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo Afilisitiwo anayamba kunena kuti: “Taonani Aheberi akutuluka m’maenje amene anabisala.”+