1 Samueli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi. 1 Samueli 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nawonso amuna onse a Isiraeli amene anali atabisala+ m’dera lamapiri la Efuraimu anamva kuti Afilisiti athawa, choncho Aisiraeliwo anayamba kuthamangitsa Afilisitiwo ndi kuwathira nkhondo.
6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.
22 Nawonso amuna onse a Isiraeli amene anali atabisala+ m’dera lamapiri la Efuraimu anamva kuti Afilisiti athawa, choncho Aisiraeliwo anayamba kuthamangitsa Afilisitiwo ndi kuwathira nkhondo.