1 Samueli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi. 1 Samueli 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero, onse awiri anadzionetsera kumudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo Afilisitiwo anayamba kunena kuti: “Taonani Aheberi akutuluka m’maenje amene anabisala.”+
6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.
11 Atatero, onse awiri anadzionetsera kumudzi wa asilikali a Afilisiti, ndipo Afilisitiwo anayamba kunena kuti: “Taonani Aheberi akutuluka m’maenje amene anabisala.”+