Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndidzakutembenuzirani dzanja langa. Ndidzasungunula zonyansa zanu zonse, ndipo ndidzachotsa nyansi zanu zonse.+

  • Ezekieli 23:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndithu, ine ndidzathetsa khalidwe lotayirira mwa iwe+ ndiponso uhule wako umene unachoka nawo kudziko la Iguputo.+ Sudzakwezanso maso ako kuyang’ana amuna a ku Iguputo ndipo dziko la Iguputo sudzalikumbukiranso.’

  • Malaki 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye adzakhala pansi ngati woyenga zitsulo ndiponso ngati woyeretsa siliva.+ Adzayeretsa ana a Levi+ ndipo adzawayeretsa ngati golide+ ndi siliva. Pamene azidzapereka nsembe zawo ngati mphatso, Yehova adzaona kuti nsembe zawozo akuzipereka+ molungama.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena