Yesaya 1:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Siliva wako wasanduka zonyansa.*+ Mowa wako wa tirigu wasukuluka ndi madzi.+ Yeremiya 6:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Onse ndi anthu ouma khosi kwambiri,+ oyenda uku ndi uku ngati anthu amiseche.+ Iwo ali ngati mkuwa ndi chitsulo. Onsewo ndi anthu owononga.+
28 Onse ndi anthu ouma khosi kwambiri,+ oyenda uku ndi uku ngati anthu amiseche.+ Iwo ali ngati mkuwa ndi chitsulo. Onsewo ndi anthu owononga.+