Maliro 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Golide amene anali kuwala, golide wabwino, sakuwalanso.+Miyala yopatulika*+ aikhuthulira m’misewu yonse.+ Ezekieli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, kwa ine a nyumba ya Isiraeli akhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo.+ Onsewo ali ngati mkuwa, tini, chitsulo ndi mtovu m’ng’anjo. Iwo akhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga siliva.+
4 Golide amene anali kuwala, golide wabwino, sakuwalanso.+Miyala yopatulika*+ aikhuthulira m’misewu yonse.+
18 “Iwe mwana wa munthu, kwa ine a nyumba ya Isiraeli akhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga zitsulo.+ Onsewo ali ngati mkuwa, tini, chitsulo ndi mtovu m’ng’anjo. Iwo akhala ngati zinthu zachabechabe zotsalira poyenga siliva.+