Maliko 12:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Iwo ndi amene amadyerera nyumba+ za akazi amasiye, ndipo mwachiphamaso amapereka mapemphero ataliatali. Anthu amenewa adzalandira chiweruzo champhamvu.”+ Luka 20:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Iwo ndi amene amadyerera nyumba za akazi amasiye,+ ndipo mwachiphamaso amapereka mapemphero ataliatali. Anthu amenewa adzalandira chiweruzo champhamvu.”+
40 Iwo ndi amene amadyerera nyumba+ za akazi amasiye, ndipo mwachiphamaso amapereka mapemphero ataliatali. Anthu amenewa adzalandira chiweruzo champhamvu.”+
47 Iwo ndi amene amadyerera nyumba za akazi amasiye,+ ndipo mwachiphamaso amapereka mapemphero ataliatali. Anthu amenewa adzalandira chiweruzo champhamvu.”+