Ezekieli 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Unawonjezera kuchita zauhule ndi dziko la Kanani+ ndiponso Akasidi.+ Ngakhale amenewanso sunakhutiritsidwe nawo.
29 Unawonjezera kuchita zauhule ndi dziko la Kanani+ ndiponso Akasidi.+ Ngakhale amenewanso sunakhutiritsidwe nawo.