Ezekieli 16:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’zonyansa zako zonse ndi m’zochita zako zauhule sunakumbukire masiku a ubwana wako pamene unali wosavala ndi wamaliseche, pamene unali kuponyaponya timiyendo tako m’mwamba uli m’magazi ako.+
22 M’zonyansa zako zonse ndi m’zochita zako zauhule sunakumbukire masiku a ubwana wako pamene unali wosavala ndi wamaliseche, pamene unali kuponyaponya timiyendo tako m’mwamba uli m’magazi ako.+