Ezekieli 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Unayamba kuchita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu a ziwalo zikuluzikulu amene ukukhala nawo pafupi.+ Unapitiriza kuwonjezera uhule wako kuti undikwiyitse.
26 Unayamba kuchita uhule ndi ana aamuna a Iguputo,+ anthu a ziwalo zikuluzikulu amene ukukhala nawo pafupi.+ Unapitiriza kuwonjezera uhule wako kuti undikwiyitse.