Ezekieli 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo+ n’kufa chifukwa cha zochita zakezo, wafa chifukwa cha zochita zake zopanda chilungamo.+ Ezekieli 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo, ayenera kufa chifukwa cha zochita zakezo.+
26 “‘Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo+ n’kufa chifukwa cha zochita zakezo, wafa chifukwa cha zochita zake zopanda chilungamo.+
18 “Munthu wolungama akasiya chilungamo chake n’kumachita zinthu zopanda chilungamo, ayenera kufa chifukwa cha zochita zakezo.+