Ezekieli 33:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno m’chaka cha 12 kuchokera pamene tinatengedwa ukapolo, m’mwezi wa 10, pa tsiku lachisanu la mweziwo, kunafika munthu amene anapulumuka kuchokera ku Yerusalemu. Iye anandiuza+ kuti: “Mzinda uja wawonongedwa!”+
21 Ndiyeno m’chaka cha 12 kuchokera pamene tinatengedwa ukapolo, m’mwezi wa 10, pa tsiku lachisanu la mweziwo, kunafika munthu amene anapulumuka kuchokera ku Yerusalemu. Iye anandiuza+ kuti: “Mzinda uja wawonongedwa!”+