Ezekieli 24:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kodi pa tsiku limenelo wothawa sadzabwera kwa iwe kuti adzanene zimene zachitika?+