Ezekieli 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkango wamphongowo unadziwa nsanja zokhalamo anthu ndipo unawononga mizinda yawo.+ Chotero dzikolo linakhala bwinja moti munkangomveka kubangula kwa mkangowo.+
7 Mkango wamphongowo unadziwa nsanja zokhalamo anthu ndipo unawononga mizinda yawo.+ Chotero dzikolo linakhala bwinja moti munkangomveka kubangula kwa mkangowo.+