1 Mafumu 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 M’zombomo, Hiramu ankatumizamo antchito ake+ omwe anali amalinyero odziwa za panyanja, pamodzi ndi antchito a Solomo.
27 M’zombomo, Hiramu ankatumizamo antchito ake+ omwe anali amalinyero odziwa za panyanja, pamodzi ndi antchito a Solomo.